2 Akorinto 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano amene anatikonzekeretsa kuti tilandire zimenezi ndi Mulungu.+ Iye ndiye anatipatsa chikole+ cha zinthu zam’tsogolo, chomwe ndi mzimu.+ Aefeso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 umene ndi chikole+ cha cholowa chathu cham’tsogolo,+ kuti anthu a Mulungu+ adzamasulidwe ndi dipo,+ n’cholinga choti iye adzatamandidwe ndi kupatsidwa ulemerero.
5 Tsopano amene anatikonzekeretsa kuti tilandire zimenezi ndi Mulungu.+ Iye ndiye anatipatsa chikole+ cha zinthu zam’tsogolo, chomwe ndi mzimu.+
14 umene ndi chikole+ cha cholowa chathu cham’tsogolo,+ kuti anthu a Mulungu+ adzamasulidwe ndi dipo,+ n’cholinga choti iye adzatamandidwe ndi kupatsidwa ulemerero.