Maliko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+ Yohane 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.
14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+
20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.