Aroma 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza imfa imene anafa, anafa kuti achotse uchimo kamodzi kokha basi,+ koma moyo umene ali nawo, akukhala nawo kuti azichita chifuniro cha Mulungu.+ Aheberi 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 n’chimodzimodzinso Khristu. Iye anaperekedwa nsembe kamodzi+ kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Ndipo nthawi yachiwiri+ imene adzaonekere+ sadzaonekera n’cholinga chochotsa uchimo.+ Anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse ndi amene adzamuone.+
10 Popeza imfa imene anafa, anafa kuti achotse uchimo kamodzi kokha basi,+ koma moyo umene ali nawo, akukhala nawo kuti azichita chifuniro cha Mulungu.+
28 n’chimodzimodzinso Khristu. Iye anaperekedwa nsembe kamodzi+ kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Ndipo nthawi yachiwiri+ imene adzaonekere+ sadzaonekera n’cholinga chochotsa uchimo.+ Anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse ndi amene adzamuone.+