Aheberi 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti Mulungu wathu alinso moto wowononga.+ 2 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndithu, Mulungu sanalekerere angelo+ amene anachimwa aja osawapatsa chilango, koma mwa kuwaponya mu Tatalasi,*+ anawaika m’maenje a mdima wandiweyani powasungira chiweruzo.+
4 Ndithu, Mulungu sanalekerere angelo+ amene anachimwa aja osawapatsa chilango, koma mwa kuwaponya mu Tatalasi,*+ anawaika m’maenje a mdima wandiweyani powasungira chiweruzo.+