Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+