Genesis 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+
9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+