Ekisodo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ ndi kuwauza kuti: “Sankhani nkhosa ndi mbuzi* malinga ndi mabanja anu, muiphere nsembe ya pasika.+
21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ ndi kuwauza kuti: “Sankhani nkhosa ndi mbuzi* malinga ndi mabanja anu, muiphere nsembe ya pasika.+