Oweruza 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi+ anakhala mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Mayi ake anali hule,+ ndipo bambo ake omubereka anali Giliyadi.
11 Tsopano Yefita+ wa ku Giliyadi+ anakhala mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Mayi ake anali hule,+ ndipo bambo ake omubereka anali Giliyadi.