Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,+Ndi kuwala kounikira njira yanga.+ Miyambo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Salaza njira ya phazi lako,+ ndipo njira zako zonse zikhazikike.+