Aefeso 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 ndipo musam’patse malo Mdyerekezi.+ Aefeso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,
11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,