Yesaya 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+ Mateyu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wakufa ziwalo, atagona pakabedi.+ Poona chikhulupiriro chawo, Yesu anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Limba mtima, mwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+
24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+
2 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wakufa ziwalo, atagona pakabedi.+ Poona chikhulupiriro chawo, Yesu anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Limba mtima, mwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+