Hoseya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ndiyeno ana a Isiraeli adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene anali kuuzidwa kuti, ‘Anthu inu sindinu anthu anga,’+ adzauzidwanso kuti, ‘Inu ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+ Machitidwe 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+ Aroma 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zilinso monga mmene ananenera m’buku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatcha ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sanali wokondedwa ndidzamutcha ‘wokondedwa.’+
10 “Ndiyeno ana a Isiraeli adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene anali kuuzidwa kuti, ‘Anthu inu sindinu anthu anga,’+ adzauzidwanso kuti, ‘Inu ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+
14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+
25 Zilinso monga mmene ananenera m’buku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatcha ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sanali wokondedwa ndidzamutcha ‘wokondedwa.’+