Yesaya 65:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 “Ine ndalola kuti anthu amene sanafunse za ine+ andifunefune.+ Ndalola kuti anthu amene sanandifunefune andipeze.+ Ndanena kuti, ‘Ndili pano, ndili pano!’+ kwa mtundu umene sunaitane pa dzina langa.+ Hoseya 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+
65 “Ine ndalola kuti anthu amene sanafunse za ine+ andifunefune.+ Ndalola kuti anthu amene sanandifunefune andipeze.+ Ndanena kuti, ‘Ndili pano, ndili pano!’+ kwa mtundu umene sunaitane pa dzina langa.+
23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+