Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,+Ndi kuwala kounikira njira yanga.+ Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwala+ kwenikweni kumene kumaunikira+ anthu osiyanasiyana+ kunali pafupi kubwera m’dziko. Yohane 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu ameneyu anali nyale yoyaka ndi yowala, ndipo kwa kanthawi kochepa inu munali ofunitsitsa kusangalala m’kuwala kwakeko.+
35 Munthu ameneyu anali nyale yoyaka ndi yowala, ndipo kwa kanthawi kochepa inu munali ofunitsitsa kusangalala m’kuwala kwakeko.+