Levitiko 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu+ ndipo sangathe kudzisamala, muzim’thandiza.+ Iye ayenera kukhala ndi moyo mmene mlendo wokhala pakati panu+ alili ndi moyo. Deuteronomo 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+ Yakobo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma wina mwa inu n’kunena kuti: “Yendani bwino, mupeze zovala ndi zakudya za tsiku lililonse,” koma osamupatsa zimene thupi lake likusowazo, kodi pali phindu lanji?+
35 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu+ ndipo sangathe kudzisamala, muzim’thandiza.+ Iye ayenera kukhala ndi moyo mmene mlendo wokhala pakati panu+ alili ndi moyo.
7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+
16 koma wina mwa inu n’kunena kuti: “Yendani bwino, mupeze zovala ndi zakudya za tsiku lililonse,” koma osamupatsa zimene thupi lake likusowazo, kodi pali phindu lanji?+