1 Akorinto 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Amene amagwiritsira ntchito dzikoli+ azikhala ngati amene sakuligwiritsira ntchito mokwanira, pakuti zochitika za padzikoli zikusintha.+ 1 Petulo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+
31 Amene amagwiritsira ntchito dzikoli+ azikhala ngati amene sakuligwiritsira ntchito mokwanira, pakuti zochitika za padzikoli zikusintha.+
24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+