2 Akorinto 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma amene amatitsimikizira kuti inuyo ndi ife tili a Khristu, amenenso anatidzoza,+ ndiye Mulungu. 1 Yohane 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munadzozedwa ndi woyerayo,+ ndipo nonsenu ndinu odziwa choonadi.+
21 Koma amene amatitsimikizira kuti inuyo ndi ife tili a Khristu, amenenso anatidzoza,+ ndiye Mulungu.