1 Yohane 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikulembera abambo inu, chifukwa mukumudziwa amene wakhala alipo kuyambira pa chiyambi.+ Ndikulemberanso inu anyamata+ chifukwa mwagonjetsa woipayo.+ Ndikulembera inu ana+ chifukwa mukuwadziwa Atate.+
13 Ndikulembera abambo inu, chifukwa mukumudziwa amene wakhala alipo kuyambira pa chiyambi.+ Ndikulemberanso inu anyamata+ chifukwa mwagonjetsa woipayo.+ Ndikulembera inu ana+ chifukwa mukuwadziwa Atate.+