Yesaya 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu ya anthu idzatsata kuwala kwako,+ ndipo mafumu+ adzatsata kunyezimira kwako.+