Chivumbulutso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+
14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+