Chivumbulutso 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ndinaona mutu wake umodzi ukuoneka kuti wavulazidwa kwambiri. Koma ngakhale kuti balalo linali loti chikanafa nalo,+ linapola. Ndipo dziko lonse lapansi linatsatira chilombocho pochita nacho chidwi.
3 Ndiyeno ndinaona mutu wake umodzi ukuoneka kuti wavulazidwa kwambiri. Koma ngakhale kuti balalo linali loti chikanafa nalo,+ linapola. Ndipo dziko lonse lapansi linatsatira chilombocho pochita nacho chidwi.