1 Petulo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ino ndiyo nthawi yoikidwiratu yakuti chiweruzo chiyambe, ndipo chiyambira panyumba ya Mulungu.+ Tsopano ngati chikuyambira pa ife,+ ndiye mapeto a anthu osamvera uthenga wabwino wa Mulungu adzakhala otani?+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
17 Pakuti ino ndiyo nthawi yoikidwiratu yakuti chiweruzo chiyambe, ndipo chiyambira panyumba ya Mulungu.+ Tsopano ngati chikuyambira pa ife,+ ndiye mapeto a anthu osamvera uthenga wabwino wa Mulungu adzakhala otani?+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+