Chivumbulutso 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa.
10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa.