Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+ 1 Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+
1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+
1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+