Genesis 41:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Komanso, anthu padziko lonse lapansi anayamba kubwera ku Iguputo kudzagula chakudya kwa Yosefe, chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.+ Machitidwe 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ku Iguputo ndi ku Kanani konse kunagwa njala moti kunali mavuto aakulu. Ndipo makolo athuwo sankapeza chakudya.+
57 Komanso, anthu padziko lonse lapansi anayamba kubwera ku Iguputo kudzagula chakudya kwa Yosefe, chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.+
11 Kenako ku Iguputo ndi ku Kanani konse kunagwa njala moti kunali mavuto aakulu. Ndipo makolo athuwo sankapeza chakudya.+