Genesis 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anati: “Akapolo anufe ndife pachibale ndipo tinalipo 12.+ Ndife ana a munthu mmodzi+ wa ku Kanani. Wamngʼono kwambiri watsala ndi bambo athu,+ koma mmodzi kulibenso.”+
13 Iwo anati: “Akapolo anufe ndife pachibale ndipo tinalipo 12.+ Ndife ana a munthu mmodzi+ wa ku Kanani. Wamngʼono kwambiri watsala ndi bambo athu,+ koma mmodzi kulibenso.”+