Genesis 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Yehova anayamba kumva fungo losangalatsa.* Choncho Yehova ananena mumtima mwake kuti: “Sindidzatembereranso nthaka+ chifukwa cha zochita za anthu, popeza maganizo a anthu amakhala oipa kuyambira ali ana.+ Ndipo sindidzaphanso chamoyo chilichonse ngati mmene ndachitiramu.+ Yeremiya 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtima ndi wopusitsa* kwambiri kuposa chinthu chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndi ndani angaudziwe? Mateyu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwachitsanzo, mumtima mumachokera maganizo oipa awa:+ maganizo a kupha anthu, a chigololo, a chiwerewere,* a kuba, maumboni onama komanso kunyoza Mulungu.
21 Ndiyeno Yehova anayamba kumva fungo losangalatsa.* Choncho Yehova ananena mumtima mwake kuti: “Sindidzatembereranso nthaka+ chifukwa cha zochita za anthu, popeza maganizo a anthu amakhala oipa kuyambira ali ana.+ Ndipo sindidzaphanso chamoyo chilichonse ngati mmene ndachitiramu.+
9 Mtima ndi wopusitsa* kwambiri kuposa chinthu chilichonse ndipo ungathe kuchita china chilichonse choipa.*+ Ndi ndani angaudziwe?
19 Mwachitsanzo, mumtima mumachokera maganizo oipa awa:+ maganizo a kupha anthu, a chigololo, a chiwerewere,* a kuba, maumboni onama komanso kunyoza Mulungu.