Genesis 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma musadzimvere chisoni kapena kuimbana mlandu kuti munandigulitsa kuno, chifukwa Mulungu ndi amene ananditumiza kuno kuti tikhalebe ndi moyo.+ Salimo 105:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu anatsogoza Yosefe,Munthu amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+
5 Koma musadzimvere chisoni kapena kuimbana mlandu kuti munandigulitsa kuno, chifukwa Mulungu ndi amene ananditumiza kuno kuti tikhalebe ndi moyo.+