Genesis 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nowa anali ndi zaka 600 pamene chigumula chinachitika padziko lapansi.+ Genesis 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mʼchaka cha 600 cha moyo wa Nowa, mʼmwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli madzi onse akumwamba anaphulika ndipo zitseko zotchingira madzi akumwamba zinatseguka.+
11 Mʼchaka cha 600 cha moyo wa Nowa, mʼmwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli madzi onse akumwamba anaphulika ndipo zitseko zotchingira madzi akumwamba zinatseguka.+