Genesis 9:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana a Nowa amene anatuluka mʼchingalawa anali Semu, Hamu ndi Yafeti.+ Patapita nthawi, Hamu anabereka Kanani.+ 19 Ana a Nowa anali atatu amenewa, ndipo anthu onse anachokera kwa iwowa nʼkufalikira padziko lonse lapansi.+
18 Ana a Nowa amene anatuluka mʼchingalawa anali Semu, Hamu ndi Yafeti.+ Patapita nthawi, Hamu anabereka Kanani.+ 19 Ana a Nowa anali atatu amenewa, ndipo anthu onse anachokera kwa iwowa nʼkufalikira padziko lonse lapansi.+