Salimo 120:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsoka kwa ine, chifukwa ndakhala mʼdziko la Meseki+ ngati mlendo. Ndimakhala mutenti pakati pa matenti a ku Kedara.+ Ezekieli 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kumeneko nʼkumene kuli Meseki ndi Tubala+ limodzi ndi magulu a anthu awo onse amene ankawatsatira. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu amene anabaidwa ndi lupanga chifukwa anachititsa kuti anthu amene akukhala mʼdziko la anthu amoyo azikhala mwamantha.
5 Tsoka kwa ine, chifukwa ndakhala mʼdziko la Meseki+ ngati mlendo. Ndimakhala mutenti pakati pa matenti a ku Kedara.+
26 Kumeneko nʼkumene kuli Meseki ndi Tubala+ limodzi ndi magulu a anthu awo onse amene ankawatsatira. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu amene anabaidwa ndi lupanga chifukwa anachititsa kuti anthu amene akukhala mʼdziko la anthu amoyo azikhala mwamantha.