Ezekieli 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chinsalu chako choyendetsera ngalawa anachipanga ndi nsalu za mitundu yosiyanasiyana zochokera ku Iguputo,Ndipo pamwamba pako anaphimbapo ndi chinsalu chopangidwa ndi ulusi wabuluu komanso ubweya wa nkhosa wapepo wochokera kuzilumba za Elisha.+
7 Chinsalu chako choyendetsera ngalawa anachipanga ndi nsalu za mitundu yosiyanasiyana zochokera ku Iguputo,Ndipo pamwamba pako anaphimbapo ndi chinsalu chopangidwa ndi ulusi wabuluu komanso ubweya wa nkhosa wapepo wochokera kuzilumba za Elisha.+