Ezekieli 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Unkachita malonda ndi amalonda a ku Sheba ndi ku Raama.+ Iwo anakupatsa mafuta onunkhira abwino kwambiri amitundu yosiyanasiyana, miyala yamtengo wapatali komanso golide posinthanitsa ndi katundu wako.+
22 Unkachita malonda ndi amalonda a ku Sheba ndi ku Raama.+ Iwo anakupatsa mafuta onunkhira abwino kwambiri amitundu yosiyanasiyana, miyala yamtengo wapatali komanso golide posinthanitsa ndi katundu wako.+