Genesis 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ili ndi buku la mbiri ya Adamu. Pa tsiku* limene Mulungu analenga Adamu, anamupanga mʼchifaniziro cha Mulungu.+ Yakobo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Lilime timaligwiritsa ntchito potamanda Yehova,* amene ndi Atate, komanso ndi lilime lomwelo timatemberera anthu amene analengedwa “mʼchifaniziro cha Mulungu.”+
5 Ili ndi buku la mbiri ya Adamu. Pa tsiku* limene Mulungu analenga Adamu, anamupanga mʼchifaniziro cha Mulungu.+
9 Lilime timaligwiritsa ntchito potamanda Yehova,* amene ndi Atate, komanso ndi lilime lomwelo timatemberera anthu amene analengedwa “mʼchifaniziro cha Mulungu.”+