Genesis 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Abulamu ananyamuka monga mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pamene ankachoka ku Harana, Abulamu anali ndi zaka 75.+ Genesis 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Angelo awiri aja anafika ku Sodomu madzulo. Loti anali atakhala pageti la mzinda wa Sodomu. Atawaona ananyamuka kukakumana nawo, ndipo anawagwadira nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ 2 Petulo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma anapulumutsa Loti yemwe anali munthu wolungama.+ Loti ankavutika kwambiri mumtima chifukwa cha khalidwe lopanda manyazi* limene anthu ophwanya malamulo ankachita.
4 Choncho Abulamu ananyamuka monga mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pamene ankachoka ku Harana, Abulamu anali ndi zaka 75.+
19 Angelo awiri aja anafika ku Sodomu madzulo. Loti anali atakhala pageti la mzinda wa Sodomu. Atawaona ananyamuka kukakumana nawo, ndipo anawagwadira nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
7 Koma anapulumutsa Loti yemwe anali munthu wolungama.+ Loti ankavutika kwambiri mumtima chifukwa cha khalidwe lopanda manyazi* limene anthu ophwanya malamulo ankachita.