Genesis 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri, mzinda wa Akasidi, kuti ndidzakupatse dzikoli likhale lako.”+ Nehemiya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ nʼkumutulutsa mumzinda wa Uri+ wa Akasidi ndipo munamupatsa dzina lakuti Abulahamu.+
7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri, mzinda wa Akasidi, kuti ndidzakupatse dzikoli likhale lako.”+
7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ nʼkumutulutsa mumzinda wa Uri+ wa Akasidi ndipo munamupatsa dzina lakuti Abulahamu.+