Genesis 10:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anakhala mlenje wamphamvu wotsutsa Yehova. Nʼchifukwa chake pali mawu akuti: “Monga Nimurodi mlenje wamphamvu wotsutsa Yehova.” 10 Ufumu wake unayambira ku* Babele,+ Ereke,+ Akadi mpaka ku Kaline mʼdziko la Sinara.+
9 Iye anakhala mlenje wamphamvu wotsutsa Yehova. Nʼchifukwa chake pali mawu akuti: “Monga Nimurodi mlenje wamphamvu wotsutsa Yehova.” 10 Ufumu wake unayambira ku* Babele,+ Ereke,+ Akadi mpaka ku Kaline mʼdziko la Sinara.+