Genesis 17:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri. 6 Ndidzakupatsa mbadwa zambirimbiri, ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu ndi mafumu.+
5 Dzina lako silikhalanso Abulamu* koma likhala Abulahamu,* chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri. 6 Ndidzakupatsa mbadwa zambirimbiri, ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu ndi mafumu.+