Genesis 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isaki atakwanitsa masiku 8, Abulahamu anachita mdulidwe wa mwana wakeyo, monga mmene Mulungu anamulamulira.+ Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+
4 Isaki atakwanitsa masiku 8, Abulahamu anachita mdulidwe wa mwana wakeyo, monga mmene Mulungu anamulamulira.+
29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+