Genesis 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno mmodzi wa iwo anati: “Ndithu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara mkazi wako adzakhala ndi mwana wamwamuna.”+ Pa nthawiyi nʼkuti Sara akumvetsera ali pakhomo la tenti imene inali kumbuyo kwa mlendoyo.
10 Ndiyeno mmodzi wa iwo anati: “Ndithu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara mkazi wako adzakhala ndi mwana wamwamuna.”+ Pa nthawiyi nʼkuti Sara akumvetsera ali pakhomo la tenti imene inali kumbuyo kwa mlendoyo.