Genesis 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mngelo wa Yehovayo ananenanso kuti: “Taona, panopa ndiwe woyembekezera, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamʼpatse dzina lakuti Isimaeli,* chifukwa Yehova wamva kulira kwako.
11 Mngelo wa Yehovayo ananenanso kuti: “Taona, panopa ndiwe woyembekezera, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamʼpatse dzina lakuti Isimaeli,* chifukwa Yehova wamva kulira kwako.