-
Genesis 2:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Zitatero Yehova Mulungu anadzala munda ku Edeni,+ chakumʼmawa, ndipo mʼmundamo anaikamo munthu amene anamuumba uja.+ 9 Choncho Yehova Mulungu anameretsa munthaka mtengo wamtundu uliwonse wooneka bwino komanso wazipatso zabwino kudya. Anameretsanso mtengo wa moyo+ pakati pa mundawo komanso mtengo wodziwitsa chabwino ndi choipa.+
-