Genesis 10:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+ Genesis 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano mʼdzikomo munagwa njala yaikulu ngati imene inagwa mʼmasiku a Abulahamu.+ Choncho Isaki anapita kwa Abimeleki, mfumu ya Afilisiti, ku Gerari.
13 Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+
26 Tsopano mʼdzikomo munagwa njala yaikulu ngati imene inagwa mʼmasiku a Abulahamu.+ Choncho Isaki anapita kwa Abimeleki, mfumu ya Afilisiti, ku Gerari.