-
Aheberi 11:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Chifukwa cha chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera nʼkupita kumalo amene ankayembekezera kuwalandira ngati cholowa. Iye anapitadi, ngakhale kuti sankadziwa kumene akupita.+ 9 Chifukwa cha chikhulupiriro, ankakhala monga mlendo mʼdziko limene analonjezedwa.+ Iye ankakhala mʼmatenti+ pamodzi ndi Isaki ndi Yakobo, amenenso Mulungu anawalonjeza kuti adzawapatsa dzikoli.+
-