Genesis 21:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anakumbukira Sara monga mmene ananenera, ndipo Yehova anachitira Sara mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ 2 Choncho Sara anakhala woyembekezera+ ndipo anaberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika ndendende pa nthawi imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+ Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, ankaganizira za thupi lake, limene pa nthawiyo linali ngati lakufa (popeza anali ndi zaka pafupifupi 100).+ Ankadziwanso kuti Sara ndi wokalamba kwambiri ndipo sangabereke mwana.+ Aheberi 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha chikhulupiriro, Sara nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa ankaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.*
21 Yehova anakumbukira Sara monga mmene ananenera, ndipo Yehova anachitira Sara mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ 2 Choncho Sara anakhala woyembekezera+ ndipo anaberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika ndendende pa nthawi imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, ankaganizira za thupi lake, limene pa nthawiyo linali ngati lakufa (popeza anali ndi zaka pafupifupi 100).+ Ankadziwanso kuti Sara ndi wokalamba kwambiri ndipo sangabereke mwana.+
11 Chifukwa cha chikhulupiriro, Sara nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa ankaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.*