Salimo 77:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzaganizira mozama za ntchito zanu zonse,Ndipo ndiziganizira mwakuya zochita zanu.+ Salimo 143:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikukumbukira masiku akale.Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.
5 Ndikukumbukira masiku akale.Ndimaganizira mozama zochita zanu zonse.+Ndimaganizira* ntchito ya manja anu ndi mtima wonse.