Genesis 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Mulungu anamuuza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo mupite ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.” Mateyu 1:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Buku la mzere wa makolo a Yesu Khristu,* mwana wa Davide,+ mwana wa Abulahamu:+ 2 Abulahamu anabereka Isaki.+Isaki anabereka Yakobo.+Yakobo anabereka Yuda+ ndi azichimwene ake.
2 Kenako Mulungu anamuuza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo mupite ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”
1 Buku la mzere wa makolo a Yesu Khristu,* mwana wa Davide,+ mwana wa Abulahamu:+ 2 Abulahamu anabereka Isaki.+Isaki anabereka Yakobo.+Yakobo anabereka Yuda+ ndi azichimwene ake.