Genesis 24:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye anati: “Ine ndine mtumiki wa Abulahamu.+ 35 Yehova wamudalitsa kwambiri mbuye wanga ndipo wamupatsa chuma chambiri moti ali ndi nkhosa, ngʼombe, siliva, golide, antchito aamuna ndi aakazi komanso ngamila ndi abulu.+
34 Iye anati: “Ine ndine mtumiki wa Abulahamu.+ 35 Yehova wamudalitsa kwambiri mbuye wanga ndipo wamupatsa chuma chambiri moti ali ndi nkhosa, ngʼombe, siliva, golide, antchito aamuna ndi aakazi komanso ngamila ndi abulu.+