Aheberi 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa cha chikhulupiriro, ankakhala monga mlendo mʼdziko limene analonjezedwa.+ Iye ankakhala mʼmatenti+ pamodzi ndi Isaki ndi Yakobo, amenenso Mulungu anawalonjeza kuti adzawapatsa dzikoli.+
9 Chifukwa cha chikhulupiriro, ankakhala monga mlendo mʼdziko limene analonjezedwa.+ Iye ankakhala mʼmatenti+ pamodzi ndi Isaki ndi Yakobo, amenenso Mulungu anawalonjeza kuti adzawapatsa dzikoli.+