-
Genesis 36:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Esau anakwatira ana aakazi a ku Kanani. Anakwatira Ada,+ mwana wamkazi wa Eloni, Muhiti.+ Anakwatiranso Oholibama,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Ana komanso anali mdzukulu wa Zibeoni, Mhivi. 3 Anakwatiranso Basemati,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Isimaeli komanso anali mchemwali wake wa Nebayoti.+
-